Yesaya 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mbewu za ku Sihori+ ndi zokolola za kumtsinje wa Nailo, zimene zinali kuyenda pamadzi ambiri ndiponso zimene zinali kukubweretserani ndalama, zakhala phindu la mitundu ina ya anthu.+
3 Mbewu za ku Sihori+ ndi zokolola za kumtsinje wa Nailo, zimene zinali kuyenda pamadzi ambiri ndiponso zimene zinali kukubweretserani ndalama, zakhala phindu la mitundu ina ya anthu.+