Ezekieli 27:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Zinthu zimene unasunga+ zikafika kumtunda+ zinali kukwanira mitundu yambiri ya anthu.+ Mafumu a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zako zochuluka zamtengo wapatali ndi katundu wako wogulitsa.+ Ezekieli 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa chakuti ndiwe wanzeru ndiponso wozindikira, wapanga chuma ndipo ukupitiriza kusonkhanitsa golide ndi siliva m’nyumba zako zosungiramo zinthu.+ Yoweli 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa chakuti anthu inu mwatenga siliva ndi golide wanga,+ mwabweretsa zinthu zanga zamtengo wapatali mu akachisi anu,+
33 Zinthu zimene unasunga+ zikafika kumtunda+ zinali kukwanira mitundu yambiri ya anthu.+ Mafumu a padziko lapansi analemera chifukwa cha zinthu zako zochuluka zamtengo wapatali ndi katundu wako wogulitsa.+
4 Chifukwa chakuti ndiwe wanzeru ndiponso wozindikira, wapanga chuma ndipo ukupitiriza kusonkhanitsa golide ndi siliva m’nyumba zako zosungiramo zinthu.+
5 Chifukwa chakuti anthu inu mwatenga siliva ndi golide wanga,+ mwabweretsa zinthu zanga zamtengo wapatali mu akachisi anu,+