2 Mbiri 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho iwo anabwera kudzalimbana nawo mpaka analowa mu Yuda. Anthuwo anatenga katundu yense amene anali m’nyumba ya mfumu,+ ana ake ndi akazi ake.+ Sanamusiyire mwana aliyense kupatulapo Yehoahazi+ mwana wake wamng’ono kwambiri.
17 Choncho iwo anabwera kudzalimbana nawo mpaka analowa mu Yuda. Anthuwo anatenga katundu yense amene anali m’nyumba ya mfumu,+ ana ake ndi akazi ake.+ Sanamusiyire mwana aliyense kupatulapo Yehoahazi+ mwana wake wamng’ono kwambiri.