Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 22:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho Yehoramu anabwerera n’kupita ku Yezereeli+ kuti akachire zilonda zimene anam’vulaza ku Rama,+ pamene anali kumenyana ndi Hazaeli mfumu ya Siriya.

      Chotero Azariya*+ mwana wa Yehoramu+ mfumu ya Yuda anapita ku Yezereeli kukaona Yehoramu+ mwana wa Ahabu chifukwa anali kudwala.+

  • 2 Mbiri 25:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yehoasi mfumu ya Isiraeli anagwira+ Amaziya mfumu ya Yuda, mwana wa Yehoasi, mwana wa Yehoahazi ku Beti-semesiko. Kenako Yehoasi anatenga Amaziya n’kupita naye ku Yerusalemu,+ ndipo anakagumula mpanda wa Yerusalemu kuyambira pa Chipata cha Efuraimu+ mpaka kukafika pa Chipata cha Pakona.+ Anagumula mpata waukulu mikono 400.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena