6 Choncho Yehoramu anabwerera nʼkupita ku Yezereeli+ kuti akachire mabala amene anamʼvulaza ku Rama, pamene ankamenyana ndi Hazaeli mfumu ya Siriya.+
Ahaziya mwana wa Yehoramu+ mfumu ya Yuda anapita ku Yezereeli kukaona Yehoramu+ mwana wa Ahabu chifukwa anali atavulazidwa.+