Yesaya 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa makamu ndi amene wapereka chigamulo chimenechi,+ kuti anyansitse kukongola kwa mzindawo ndi kuchotsa kunyada kwake,+ ndiponso kuti anyoze anthu onse olemekezeka a padziko lapansi.+
9 Yehova wa makamu ndi amene wapereka chigamulo chimenechi,+ kuti anyansitse kukongola kwa mzindawo ndi kuchotsa kunyada kwake,+ ndiponso kuti anyoze anthu onse olemekezeka a padziko lapansi.+