Yeremiya 51:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 “Chotero masiku adzafika,” watero Yehova, “ndipo ndidzalanga zifaniziro zake zogoba.+ M’dziko lake lonse anthu obayidwa adzakhala akubuula.”+
52 “Chotero masiku adzafika,” watero Yehova, “ndipo ndidzalanga zifaniziro zake zogoba.+ M’dziko lake lonse anthu obayidwa adzakhala akubuula.”+