Yesaya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale mitengo ya mlombwa+ yakondwa poona zimene zakuchitikira. Nayonso mitengo ya mkungudza ya ku Lebanoni yakondwa, ndipo yonseyi yanena kuti, ‘Kuyambira pamene unagona pansi, palibenso munthu wodula mitengo+ amene wabwera kudzatidula.’ Ezekieli 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mtengo umenewu ndinaukongoletsa pouchulukitsira nthambi zamasamba ambiri.+ Mitengo ina yonse ya mu Edeni, imene inali m’munda wa Mulungu woona, inali kuuchitira nsanje.’+
8 Ngakhale mitengo ya mlombwa+ yakondwa poona zimene zakuchitikira. Nayonso mitengo ya mkungudza ya ku Lebanoni yakondwa, ndipo yonseyi yanena kuti, ‘Kuyambira pamene unagona pansi, palibenso munthu wodula mitengo+ amene wabwera kudzatidula.’
9 Mtengo umenewu ndinaukongoletsa pouchulukitsira nthambi zamasamba ambiri.+ Mitengo ina yonse ya mu Edeni, imene inali m’munda wa Mulungu woona, inali kuuchitira nsanje.’+