Ezekieli 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “‘Amenewa ndiwo anthu amene Farao adzawaone ndipo mtima wake udzakhala pansi poona khamu lake lonse.+ Farao ndi gulu lake lonse lankhondo adzakhala m’gulu la anthu ophedwa ndi lupanga,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
31 “‘Amenewa ndiwo anthu amene Farao adzawaone ndipo mtima wake udzakhala pansi poona khamu lake lonse.+ Farao ndi gulu lake lonse lankhondo adzakhala m’gulu la anthu ophedwa ndi lupanga,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.