-
Ezekieli 31:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Mitundu ya anthu ikadzamva phokoso la kugwa kwake idzanjenjemera. Zimenezi zidzachitika ndikadzatsitsira mtengowo ku Manda pamodzi ndi amene akutsikira kudzenje.+ Mitengo yonse ya mu Edeni+ imene ili pansi pa nthaka, mitengo yabwino kwambiri ya ku Lebanoni ndi mitengo yonse imene inali pamadzi ambiri, idzatonthozedwa.+
-