Ezekieli 29:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndibweretsa lupanga+ m’dziko lako ndipo ndidzapha anthu ndi ziweto.+ Ezekieli 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzaumitsa ngalande zotuluka mumtsinje wa Nailo+ ndi kugulitsa dzikolo kwa anthu oipa.+ Ndidzachititsa kuti dzikolo ndi zonse zimene zili mmenemo ziwonongedwe ndi anthu achilendo.+ Ine Yehova, ndanena zimenezi.’+
8 “‘Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndibweretsa lupanga+ m’dziko lako ndipo ndidzapha anthu ndi ziweto.+
12 Ndidzaumitsa ngalande zotuluka mumtsinje wa Nailo+ ndi kugulitsa dzikolo kwa anthu oipa.+ Ndidzachititsa kuti dzikolo ndi zonse zimene zili mmenemo ziwonongedwe ndi anthu achilendo.+ Ine Yehova, ndanena zimenezi.’+