Yesaya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo mserafi mmodzi anaulukira kwa ine. M’manja mwake munali khala lamoto+ limene analitenga paguwa lansembe ndi chopanira.+ Ezekieli 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kupansi kwa mapiko a akerubiwo,+ kunaoneka chinachake chokhala ngati dzanja la munthu.
6 Pamenepo mserafi mmodzi anaulukira kwa ine. M’manja mwake munali khala lamoto+ limene analitenga paguwa lansembe ndi chopanira.+