Ezekieli 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anandiuzanso kuti: “Iwe mwana wa munthu, mafupawa akuimira nyumba yonse ya Isiraeli.+ Iwo akunena kuti, ‘Mafupa athu auma ndipo tilibenso chiyembekezo chilichonse.+ Atilekanitsa ndi anzathu ndipo tili kwatokhatokha.’
11 Iye anandiuzanso kuti: “Iwe mwana wa munthu, mafupawa akuimira nyumba yonse ya Isiraeli.+ Iwo akunena kuti, ‘Mafupa athu auma ndipo tilibenso chiyembekezo chilichonse.+ Atilekanitsa ndi anzathu ndipo tili kwatokhatokha.’