Salimo 141:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mafupa athu amwazika pakamwa pa Manda,Mofanana ndi zidutswa zimene zimamwazika pansi pamene munthu akuwaza ndi kung’amba mtengo.+ Yesaya 49:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Ziyoni ankangonena kuti: “Yehova wandisiya+ ndipo Yehova wandiiwala.”+
7 Mafupa athu amwazika pakamwa pa Manda,Mofanana ndi zidutswa zimene zimamwazika pansi pamene munthu akuwaza ndi kung’amba mtengo.+