Yeremiya 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndinaona mapiri ndipo anali kugwedezeka. Zitunda zonse zinali kunjenjemera.+ Nahumu 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapiri agwedezeka chifukwa cha iye ndipo zitunda zasungunuka.+ Dziko lapansi, nthaka ndi zinthu zonse zokhala m’dzikomo zidzanjenjemera.+
5 Mapiri agwedezeka chifukwa cha iye ndipo zitunda zasungunuka.+ Dziko lapansi, nthaka ndi zinthu zonse zokhala m’dzikomo zidzanjenjemera.+