Yesaya 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova wa makamu adzatembenukira kwa iwe kuti akupulumutse ndi mabingu, zivomezi, phokoso lalikulu, mphepo yamkuntho, ndi lawi la moto wowononga.”+ Yesaya 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+
6 Yehova wa makamu adzatembenukira kwa iwe kuti akupulumutse ndi mabingu, zivomezi, phokoso lalikulu, mphepo yamkuntho, ndi lawi la moto wowononga.”+
30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+