Ezekieli 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Kapenanso nditati nditumize mliri m’dzikolo,+ n’kukhuthulira mkwiyo wanga padzikolo, n’kukhetsa magazi+ ambiri popha anthu ndi ziweto m’dzikolo,
19 “‘Kapenanso nditati nditumize mliri m’dzikolo,+ n’kukhuthulira mkwiyo wanga padzikolo, n’kukhetsa magazi+ ambiri popha anthu ndi ziweto m’dzikolo,