Ezekieli 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uuze dziko la Isiraeli kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ine ndidzakulanga.+ Ndidzasolola lupanga langa m’chimake+ ndi kupha anthu ako olungama ndiponso anthu ako oipa.+
3 Uuze dziko la Isiraeli kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ine ndidzakulanga.+ Ndidzasolola lupanga langa m’chimake+ ndi kupha anthu ako olungama ndiponso anthu ako oipa.+