Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 30:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 “Upange guwa lansembe la zofukiza.+ Ulipange ndi matabwa a mthethe.

  • 1 Mafumu 7:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 M’kupita kwa nthawi, Solomo anapanga ziwiya zonse za panyumba ya Yehova, za paguwa lansembe+ lagolide, ndi za patebulo+ limene ankaikapo mkate wachionetsero.

  • 2 Mbiri 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Solomo anapanga ziwiya zonse+ zimene zinali panyumba ya Mulungu woona, guwa lansembe lagolide,+ matebulo+ oikapo mkate wachionetsero,

  • Chivumbulutso 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mngelo wina anafika ndi kuimirira kuguwa+ lansembe. Iye anali ndi chiwiya chofukiziramo chagolide, ndipo anamupatsa zofukiza zambiri+ kuti azipereke nsembe limodzi ndi mapemphero a oyera onse paguwa lansembe lagolide, limene linali pamaso pa mpando wachifumu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena