Ezekieli 44:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Iwo ndi amene adzalowe m’malo anga opatulika,+ ndipo adzayandikira tebulo* langa ndi kunditumikira.+ Amenewa adzachita utumiki wawo kwa ine.+ Malaki 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Mwalinyoza mwa kupereka nsembe zodetsedwa paguwa langa lansembe.’+ “‘Inu mukunena kuti: “Takudetsani motani?”’ “‘Mwandidetsa ponena kuti: “Tebulo+ la Yehova ndi lonyozeka.”+
16 ‘Iwo ndi amene adzalowe m’malo anga opatulika,+ ndipo adzayandikira tebulo* langa ndi kunditumikira.+ Amenewa adzachita utumiki wawo kwa ine.+
7 “‘Mwalinyoza mwa kupereka nsembe zodetsedwa paguwa langa lansembe.’+ “‘Inu mukunena kuti: “Takudetsani motani?”’ “‘Mwandidetsa ponena kuti: “Tebulo+ la Yehova ndi lonyozeka.”+