Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 41:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kunali guwa lansembe lamatabwa lalitali mikono itatu kuchokera pansi kufika pamwamba. M’litali mwake munali mikono iwiri ndipo m’makona ake munali mwa matabwa.+ M’litali mwa guwalo ndi m’mbali mwake munali mwa matabwa. Ndiyeno munthu uja anandiuza kuti: “Ili ndi tebulo limene lili pamaso pa Yehova.”+

  • Malaki 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “‘Mwalinyoza mwa kupereka nsembe zodetsedwa paguwa langa lansembe.’+

      “‘Inu mukunena kuti: “Takudetsani motani?”’

      “‘Mwandidetsa ponena kuti: “Tebulo+ la Yehova ndi lonyozeka.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena