Ezekieli 45:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamalo amenewa padzakhale malo oyera okwana mikono 500 m’litali ndi mikono 500 m’lifupi. Malowa adzakhale ofanana mbali zonse.+ Kumbali zake zonse kudzakhale malo odyetserako ziweto okwana mikono 50.+
2 Pamalo amenewa padzakhale malo oyera okwana mikono 500 m’litali ndi mikono 500 m’lifupi. Malowa adzakhale ofanana mbali zonse.+ Kumbali zake zonse kudzakhale malo odyetserako ziweto okwana mikono 50.+