Ezekieli 42:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anayeza malo onsewo mbali zonse zinayi. Malo onsewo anali ndi mpanda+ wokwana mabango 500 m’litali ndi mabango 500 m’lifupi mwake.+ Mpandawo unali kusiyanitsa zinthu zopatulika ndi zinthu zodetsedwa.+
20 Anayeza malo onsewo mbali zonse zinayi. Malo onsewo anali ndi mpanda+ wokwana mabango 500 m’litali ndi mabango 500 m’lifupi mwake.+ Mpandawo unali kusiyanitsa zinthu zopatulika ndi zinthu zodetsedwa.+