-
Mika 1:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Zifaniziro zake zonse zogoba zidzaphwanyidwa n’kukhala zidutswazidutswa+ ndipo mphatso zonse zimene ankalandira monga malipiro zidzatenthedwa pamoto.+ Mafano ake onse ndidzawawononga. Samariya anapeza zinthu zonsezi ndi ndalama zimene anapeza pochita uhule. Ndipo tsopano zitengedwa kuti zikakhale malipiro a mahule kwinakwake.”+
-