Ekisodo 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo anaona Mulungu wa Isiraeli.+ Pansi pa mapazi ake panali chinthu chooneka ngati miyala ya safiro yoyalidwa bwino, choyera ngati kumwamba.+ Ezekieli 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko ndinaona ulemerero+ wa Mulungu wa Isiraeli ukubwera kuchokera kumbali ya kum’mawa.+ Mawu ake anali kumveka ngati mkokomo wa madzi ambiri,+ ndipo dziko lapansi linawala chifukwa cha ulemerero wake.+
10 ndipo anaona Mulungu wa Isiraeli.+ Pansi pa mapazi ake panali chinthu chooneka ngati miyala ya safiro yoyalidwa bwino, choyera ngati kumwamba.+
2 Kumeneko ndinaona ulemerero+ wa Mulungu wa Isiraeli ukubwera kuchokera kumbali ya kum’mawa.+ Mawu ake anali kumveka ngati mkokomo wa madzi ambiri,+ ndipo dziko lapansi linawala chifukwa cha ulemerero wake.+