Levitiko 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Azikhala oyera kwa Mulungu wawo+ ndipo asaipitse dzina la Mulungu wawo,+ chifukwa iwowa amapereka nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, mkate wa Mulungu wawo,+ choncho azikhala oyera.+ Malaki 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Mwalinyoza mwa kupereka nsembe zodetsedwa paguwa langa lansembe.’+ “‘Inu mukunena kuti: “Takudetsani motani?”’ “‘Mwandidetsa ponena kuti: “Tebulo+ la Yehova ndi lonyozeka.”+
6 Azikhala oyera kwa Mulungu wawo+ ndipo asaipitse dzina la Mulungu wawo,+ chifukwa iwowa amapereka nsembe zotentha ndi moto zoperekedwa kwa Yehova, mkate wa Mulungu wawo,+ choncho azikhala oyera.+
7 “‘Mwalinyoza mwa kupereka nsembe zodetsedwa paguwa langa lansembe.’+ “‘Inu mukunena kuti: “Takudetsani motani?”’ “‘Mwandidetsa ponena kuti: “Tebulo+ la Yehova ndi lonyozeka.”+