Yoswa 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anagawira cholowacho mafuko 9 ndi hafu, mwa kuchita maere,+ monga mmene Yehova analamulira kudzera mwa Mose.+ Ezekieli 47:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mugawane dzikoli kuti likhale cholowa chanu+ ndi cha alendo okhala pakati panu, amene abereka ana pakati panu.+ Alendowo akhale ngati nzika pakati pa ana a Isiraeli. Iwo apatsidwe cholowa pamodzi ndi inu pakati pa mafuko a Isiraeli.+
2 Anagawira cholowacho mafuko 9 ndi hafu, mwa kuchita maere,+ monga mmene Yehova analamulira kudzera mwa Mose.+
22 Mugawane dzikoli kuti likhale cholowa chanu+ ndi cha alendo okhala pakati panu, amene abereka ana pakati panu.+ Alendowo akhale ngati nzika pakati pa ana a Isiraeli. Iwo apatsidwe cholowa pamodzi ndi inu pakati pa mafuko a Isiraeli.+