Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 48:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Gawo limeneli likhale chopereka chopatulika cha ansembe.+ Mbali ya kumpoto, gawoli likhale mikono 25,000 m’litali mwake. Mbali ya kumadzulo likhale mikono 10,000 m’lifupi. Mbali ya kum’mawa likhale mikono 10,000 m’lifupi, ndipo mbali ya kum’mwera gawoli likhale mikono 25,000 m’litali. Pakati pa gawo limeneli pakhale malo opatulika a Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena