Ezekieli 48:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Malo otsala okwana mikono 5,000 m’lifupi ndi mikono 25,000 m’litali, akhale malo odetsedwa a mzinda.+ Malo amenewa akhale okhalamo anthu ndi odyetserako ziweto. Pakati pa malowa pakhale mzinda.+
15 “Malo otsala okwana mikono 5,000 m’lifupi ndi mikono 25,000 m’litali, akhale malo odetsedwa a mzinda.+ Malo amenewa akhale okhalamo anthu ndi odyetserako ziweto. Pakati pa malowa pakhale mzinda.+