Ezekieli 45:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Anthu inu mudzapereke malo okwana mikono 5,000 m’lifupi ndi mikono 25,000 m’litali kuti adzakhale malo a mzinda. Malo amenewa adzakhale moyandikana ndi chopereka chopatulika,+ ndipo adzakhale a anthu a nyumba yonse ya Isiraeli.
6 “‘Anthu inu mudzapereke malo okwana mikono 5,000 m’lifupi ndi mikono 25,000 m’litali kuti adzakhale malo a mzinda. Malo amenewa adzakhale moyandikana ndi chopereka chopatulika,+ ndipo adzakhale a anthu a nyumba yonse ya Isiraeli.