Levitiko 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye aziika dzanja lake pamutu pa nsembe yopserezayo ndipo idzalandiridwa+ kuti iphimbe machimo ake.+ Levitiko 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma musadye nyama ya nsembe yamachimo imene ena mwa magazi+ ake adzalowa nawo m’chihema chokumanako kuti aphimbire machimo m’malo oyerawo. Imeneyo muziitentha ndi moto. Aheberi 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inde, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ malinga ndi Chilamulo, ndipo popanda kukhetsa magazi+ anthu sangakhululukidwe machimo awo.+
4 Iye aziika dzanja lake pamutu pa nsembe yopserezayo ndipo idzalandiridwa+ kuti iphimbe machimo ake.+
30 Koma musadye nyama ya nsembe yamachimo imene ena mwa magazi+ ake adzalowa nawo m’chihema chokumanako kuti aphimbire machimo m’malo oyerawo. Imeneyo muziitentha ndi moto.
22 Inde, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ malinga ndi Chilamulo, ndipo popanda kukhetsa magazi+ anthu sangakhululukidwe machimo awo.+