Ezekieli 45:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa tsiku limeneli, mtsogoleri azipereka kwa ansembe ng’ombe yaing’ono yamphongo kuti ikhale nsembe yamachimo ake ndi a anthu onse a m’dzikoli.+
22 Pa tsiku limeneli, mtsogoleri azipereka kwa ansembe ng’ombe yaing’ono yamphongo kuti ikhale nsembe yamachimo ake ndi a anthu onse a m’dzikoli.+