-
Ezara 6:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Komanso muziwapatsa zinthu zofunika monga ng’ombe zing’onozing’ono zamphongo,+ nkhosa zamphongo,+ ndi ana a nkhosa+ kuti azipereka nsembe yopsereza kwa Mulungu wakumwamba. Muziwapatsanso tirigu,+ mchere,+ vinyo+ ndi mafuta+ monga mmene anganenere ansembe amene ali ku Yerusalemu. Musalephere kuwapatsa zinthu zimenezi tsiku ndi tsiku mosalekeza.
-