Levitiko 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Ngati munthu aliyense pakati panu wachimwa mwa kuchita mwangozi chimodzi mwa zinthu zimene Yehova analamula kuti asachite ndipo wapalamula,+ Salimo 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndani angazindikire yekha zinthu zimene walakwitsa?+Mundikhululukire machimo amene ndachita mosadziwa.+
27 “‘Ngati munthu aliyense pakati panu wachimwa mwa kuchita mwangozi chimodzi mwa zinthu zimene Yehova analamula kuti asachite ndipo wapalamula,+
12 Ndani angazindikire yekha zinthu zimene walakwitsa?+Mundikhululukire machimo amene ndachita mosadziwa.+