Ezekieli 46:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Popereka nkhosa yamphongo aziperekanso nsembe yambewu yokwana muyezo wa efa.+ Popereka ana a nkhosa amphongo aziperekanso nsembe yambewu imene angakwanitse.+ Pa nsembe iliyonse yambewu yokwana muyezo wa efa azipereka mafuta okwana muyezo wa hini.+
5 Popereka nkhosa yamphongo aziperekanso nsembe yambewu yokwana muyezo wa efa.+ Popereka ana a nkhosa amphongo aziperekanso nsembe yambewu imene angakwanitse.+ Pa nsembe iliyonse yambewu yokwana muyezo wa efa azipereka mafuta okwana muyezo wa hini.+