Levitiko 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 m’mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova chikondwerero cha misasa kwa masiku 7.+ 2 Mbiri 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho anthu onse a mu Isiraeli anasonkhana kwa mfumu pachikondwerero cha m’mwezi wa 7.+
34 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 m’mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova chikondwerero cha misasa kwa masiku 7.+