Levitiko 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 m’mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova chikondwerero cha misasa kwa masiku 7.+ 1 Mafumu 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho anthu onse a mu Isiraeli anasonkhana kwa Mfumu Solomo pachikondwerero+ cha m’mwezi wa Etanimu, womwe ndi mwezi wa 7.+ 2 Mbiri 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi imeneyo Solomo anachita chikondwerero+ masiku 7 pamodzi ndi Aisiraeli onse.+ Unali mpingo waukulu+ wa anthu amene anachokera kumadera osiyanasiyana, kuyambira polowera ku Hamati+ n’kutsetsereka mpaka kukafika kuchigwa* cha Iguputo.+
34 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 m’mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova chikondwerero cha misasa kwa masiku 7.+
2 Choncho anthu onse a mu Isiraeli anasonkhana kwa Mfumu Solomo pachikondwerero+ cha m’mwezi wa Etanimu, womwe ndi mwezi wa 7.+
8 Pa nthawi imeneyo Solomo anachita chikondwerero+ masiku 7 pamodzi ndi Aisiraeli onse.+ Unali mpingo waukulu+ wa anthu amene anachokera kumadera osiyanasiyana, kuyambira polowera ku Hamati+ n’kutsetsereka mpaka kukafika kuchigwa* cha Iguputo.+