Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 16:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “M’mwezi wa 7, pa tsiku la 10 la mweziwo,+ muzidzisautsa*+ ndipo aliyense wa inu asamagwire ntchito ina iliyonse,+ kaya ndi nzika kapena mlendo wokhala pakati panu. Limeneli likhale lamulo kwa inu mpaka kalekale.+

  • Levitiko 23:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Tsiku la 15 m’mwezi wa 7 umenewu, ndi tsiku lochitira Yehova chikondwerero cha misasa kwa masiku 7.+

  • Deuteronomo 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Uzichita chikondwerero cha misasa+ masiku 7, potuta zokolola kuchokera pamalo opunthira mbewu, pamalo oyengera mafuta ndi pamalo opondera mphesa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena