Ezekieli 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndikadzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndi kumayiko ena, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+ Ezekieli 38:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzadzilemekeza, kudziyeretsa+ ndi kuchititsa kuti mitundu yambiri ya anthu indidziwe, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+
15 Ndikadzawabalalitsira ku mitundu ina ya anthu ndi kumayiko ena, iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.+
23 Ndidzadzilemekeza, kudziyeretsa+ ndi kuchititsa kuti mitundu yambiri ya anthu indidziwe, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+