24 Popereka ng’ombe iliyonse yaing’ono yamphongo aziperekanso nsembe yambewu yokwana muyezo wa efa. Popereka nkhosa iliyonse yamphongo aziperekanso nsembe yambewu yokwana muyezo wa efa. Pa muyezo uliwonse wa efa azipereka mafuta okwana muyezo wa hini.+