Genesis 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Usiku iye anagawa m’magulu asilikali akewo,+ omwe anali akapolo ake, kuti amenyane ndi adaniwo. Ndipo anawagonjetsa, moti anawapitikitsa mpaka ku Hoba, kumpoto kwa Damasiko.
15 Usiku iye anagawa m’magulu asilikali akewo,+ omwe anali akapolo ake, kuti amenyane ndi adaniwo. Ndipo anawagonjetsa, moti anawapitikitsa mpaka ku Hoba, kumpoto kwa Damasiko.