Numeri 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Malirewo akafike ku Zifironi, mpaka ku Hazara-enani.+ Awa ndiwo adzakhale malire anu a kumpoto.