Ezekieli 48:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Malire a kum’mwera a dzikolo akhale malire a gawo la fuko la Gadi a mbali ya kum’mwera. Malirewo achokere ku Tamara+ kukafika kumadzi a Meribati-kadesi,+ kuchigwa+ cha Iguputo, mpaka ku Nyanja Yaikulu.+
28 Malire a kum’mwera a dzikolo akhale malire a gawo la fuko la Gadi a mbali ya kum’mwera. Malirewo achokere ku Tamara+ kukafika kumadzi a Meribati-kadesi,+ kuchigwa+ cha Iguputo, mpaka ku Nyanja Yaikulu.+