Ezekieli 47:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Malire a mbali ya kum’mwera, ayambire ku Tamara+ kukafika kumadzi a Meribati-kadesi,+ kuchigwa*+ cha Iguputo mpaka ku Nyanja Yaikulu. Amenewa akhale malire a mbali ya kum’mwera, cha ku Negebu.
19 “Malire a mbali ya kum’mwera, ayambire ku Tamara+ kukafika kumadzi a Meribati-kadesi,+ kuchigwa*+ cha Iguputo mpaka ku Nyanja Yaikulu. Amenewa akhale malire a mbali ya kum’mwera, cha ku Negebu.