Numeri 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Madzi amenewo anatchedwa madzi a ku Meriba,*+ chifukwa pamalopo ana a Isiraeli anakanganapo ndi Yehova, ndipo iye anakwezeka pakati pawo. Deuteronomo 32:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Izi zili choncho chifukwa anthu inu munachita mosakhulupirika kwa ine+ pakati pa ana a Isiraeli, kumadzi a pa Meriba+ ku Kadesi, m’chipululu cha Zini. Ndiponso chifukwa chakuti anthu inu simunandilemekeze pakati pa ana a Isiraeli.+ Salimo 81:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi ya nsautso unaitana ndipo ine ndinakupulumutsa.+Ndinayamba kukuyankha m’malo obisika a bingu.+Ndinakusanthula pamadzi a Meriba.+ [Seʹlah.]
13 Madzi amenewo anatchedwa madzi a ku Meriba,*+ chifukwa pamalopo ana a Isiraeli anakanganapo ndi Yehova, ndipo iye anakwezeka pakati pawo.
51 Izi zili choncho chifukwa anthu inu munachita mosakhulupirika kwa ine+ pakati pa ana a Isiraeli, kumadzi a pa Meriba+ ku Kadesi, m’chipululu cha Zini. Ndiponso chifukwa chakuti anthu inu simunandilemekeze pakati pa ana a Isiraeli.+
7 Pa nthawi ya nsautso unaitana ndipo ine ndinakupulumutsa.+Ndinayamba kukuyankha m’malo obisika a bingu.+Ndinakusanthula pamadzi a Meriba.+ [Seʹlah.]