Salimo 81:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene unkakumana ndi mavuto unaitana, ndipo ine ndinakupulumutsa.+Ndinakuyankha ndi mabingu ochokera mumtambo.*+ Ndinakuyesa pamadzi a ku Meriba.*+ (Selah)
7 Pamene unkakumana ndi mavuto unaitana, ndipo ine ndinakupulumutsa.+Ndinakuyankha ndi mabingu ochokera mumtambo.*+ Ndinakuyesa pamadzi a ku Meriba.*+ (Selah)