Salimo 81:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawi ya nsautso unaitana ndipo ine ndinakupulumutsa.+Ndinayamba kukuyankha m’malo obisika a bingu.+Ndinakusanthula pamadzi a Meriba.+ [Seʹlah.]
7 Pa nthawi ya nsautso unaitana ndipo ine ndinakupulumutsa.+Ndinayamba kukuyankha m’malo obisika a bingu.+Ndinakusanthula pamadzi a Meriba.+ [Seʹlah.]