Ekisodo 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Farao atafika pafupi, Aisiraeli anakweza maso awo ndipo anaona Aiguputo akuwathamangira. Choncho Aisiraeli anachita mantha kwambiri ndipo anayamba kufuulira Yehova.+ Ekisodo 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atatero Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Limbani mtima ndipo muona mmene Yehova akupulumutsireni lero.+ Chifukwa Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso mpaka kalekale.+ Salimo 91:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+ Ndidzakhala naye pa nthawi ya mavuto.+ Ndidzamupulumutsa komanso kumupatsa ulemerero.
10 Farao atafika pafupi, Aisiraeli anakweza maso awo ndipo anaona Aiguputo akuwathamangira. Choncho Aisiraeli anachita mantha kwambiri ndipo anayamba kufuulira Yehova.+
13 Atatero Mose anauza anthuwo kuti: “Musachite mantha.+ Limbani mtima ndipo muona mmene Yehova akupulumutsireni lero.+ Chifukwa Aiguputo amene mukuwaona lerowa simudzawaonanso mpaka kalekale.+
15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+ Ndidzakhala naye pa nthawi ya mavuto.+ Ndidzamupulumutsa komanso kumupatsa ulemerero.