Ezekieli 47:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Malire ochokera kunyanja akafike ku Hazara-enoni,+ kumene ndi kumalire a Damasiko, mpaka kukafika kumpoto kwake, komanso kumalire a Hamati.+ Amenewa akhale malire a mbali ya kumpoto.
17 Malire ochokera kunyanja akafike ku Hazara-enoni,+ kumene ndi kumalire a Damasiko, mpaka kukafika kumpoto kwake, komanso kumalire a Hamati.+ Amenewa akhale malire a mbali ya kumpoto.