2 Mafumu 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa chifukwa chimenechi Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikubweretsa tsoka pa Yerusalemu+ ndi Yuda loti aliyense akamva, adzadabwa kwambiri.*+ Danieli 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu munachitadi zimene munachenjeza kuti mudzatichitira,+ ifeyo ndi atsogoleri athu.+ Munatigwetsera tsoka lalikulu ndipo tsoka limene lagwera Yerusalemu silinachitikeponso padziko lonse lapansi.+
12 Pa chifukwa chimenechi Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Ndikubweretsa tsoka pa Yerusalemu+ ndi Yuda loti aliyense akamva, adzadabwa kwambiri.*+
12 Inu munachitadi zimene munachenjeza kuti mudzatichitira,+ ifeyo ndi atsogoleri athu.+ Munatigwetsera tsoka lalikulu ndipo tsoka limene lagwera Yerusalemu silinachitikeponso padziko lonse lapansi.+